Watch DRIEMO – COMPENSATION (OFFICIAL VISUAL)

Post was last updated: March 13, 2023

Driemo COMPENSATION Lyrics

Intro

Kuti mwina compensation
Driemo
Ndidzapereke moyo wanga

Verse1

Oh mtima uwupereke, kwaine ndiwutenge
Don’t you worry about safety
Ndidzachengetera chengetera chengetera

I know mtima unaswekapo
You’ve been there unalirapo, ululu mumtima kufikapo
Ukaganizira ganizira ganizira
Paiwe ndilola ndipepere, chikondi chisaperewere
Olo pa ground paterere I will love you the same baby

Hook

Oh udzandifunse
Ndikadzakuswera mtima udzandifunse
Kuti mwina compensation
Ndidzapereke moyo wanga x2

Verse2

Don’t be scared to love me more
Zakale zapita it’s me and you
Undiuze pomwe Pali mantha ako

I know mtima umakana ukandiunika
Umaona ngati Aja anakunamiza koma

I wanna be your soldier
Your fighter
Protector
Defender
I just wanna be your friend for life

Hook

Oh udzandifunse
Ndikadzakuswera mtima udzandifunse
Kuti mwina compensation
Ndidzapereke moyo wanga x2

Bridge

Ooh udzandifunse
Udzandifunse, mwina compensation ndidzapereke moyo wanga eeee

Hook

Oh udzandifunse
Ndikadzakuswera mtima udzandifunse
Kuti mwina compensation
Ndidzapereke moyo wanga x2

This DRIEMO – COMPENSATION (OFFICIAL VISUAL) was first released on: 2022-07-12 20:03:53.

You can also enjoy some Driemo pictures read Driemo’s biography and discover more Malawian artists.